![Jimmy](/img/default-banner.jpg)
- 3 300
- 5 779 879
Jimmy
Приєднався 24 тра 2021
Digital marketing platform and News Update..
Відео
ZOMWE PRESIDENT RAZARUS CHAKWERA WALANKHULA LERO
Переглядів 12417 годин тому
Tamvani izi abale ....zakumalawi
AMAYI OZIDALIRA MWA IWO OKHA, TAONANI ZOMWE AKUCHITA
Переглядів 11514 годин тому
AMAYI OZIDALIRA MWA IWO OKHA, TAONANI ZOMWE AKUCHITA
ANTHU ENA AKUFUNA AZIKHALE NG'OMA ACHOSEDWE..TAMVANI ZAMBIRI
Переглядів 28014 годин тому
ANTHU ENA AKUFUNA AZIKHALE NG'OMA ACHOSEDWE..TAMVANI ZAMBIRI
ZOMWE AYANKHULA AUNDULE MWAKASUNGULA....
Переглядів 4314 годин тому
ZOMWE AYANKHULA AUNDULE MWAKASUNGULA....
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH THE BRITISH HIGH COMMISSIONER
Переглядів 1514 годин тому
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH THE BRITISH HIGH COMMISSIONER
How wi do
Tufuna za chifunga ife osati izizi ayi
Nice
Here there is no reason kut banja lithe coz bambowa nawonso atayamba kumwa mankhwala sadawauze akazi awowa ay that is means kut chifukwa chomwe bambowa sadawaziwisile akaz awowa ndchomwenso mayiwa samawaziwisila amuna awowa
Tiziyakhulanapo chichewa apa
Eee komatu
Boma ndilomweli Dr Chakwela is a man of integrity, keep up Mr president.
Nde tidziwa bwanji kuti chigamulo chinali bwanji?
Chumacho ampaseko mwanayo
Ndale basi, Kufuna kupusitsa amalawi , Adziti aimeso , Za ziiiii
Kma poti ana akazi alibe ntchitopo akurakwisa ana ndi ana zilibe ntchito kt ndiakazi or aamuna
Abale koma ma passport akutuluka kapena ayi
To the world ❤
Nyama inamuwawa mpakan kubwelera
More fire 🔥
Ndere imwe
Ndebwanji mwanayo akufanana ndi mayi omupezayo
Next
Targe me pa chigamulo day🤸🤸🤸
Asumilana anakamozi? Pansana pawo ndithu
Mwana wa mamuna akufunikila gawo lake chifukwa iwo anavomeleza poyamba
Waiting for next part
Nkhan inayamba bwinobwino kenako Mwana wakazi zalakwika
Mwanayu ndi wa m'ng'ono akuyenera kusamalidwa aphunzire school yabwino azigona pabwino chuma adzapanga yekha msogolo m'mayi wa mkuluyi wavuta sapereka gawo la chuma komanso bamboyu analakwitsa osalemba will iyeyo ndiyemwe anayenera kugawa chuma adakali ndi moyo azibambo anzanga tiphunzirepo apa nkhani izi always zimavuta kwambiri
Atambwali okhaokha awa
Mbambande Zedi Mr Phiri❤❤❤ Amen
Nkhani ili pokuti amayi akulu anavomera pachiyambi nde sangasinthe zochita poti abambo wo amwalira
Akadzutse abambo ampatse zomwe akufunazo dziko Palibe mwana wamukazi Palibe wamuna onse ndiana iya akufuna kumba uyu
Mayi wanga wan'kulu inuyo n'tchito imene munamulola mwamuna wanuyo kut aigwire asanamwalile kwazakoyo imene inuyo munaikanika kuikwaniritsa ponyozer phatso ya ana aakazi amène Mulungu anakupatsani ponena kt mukufuna wamwamuna ndiye muyener kumugawir nzanuyo pa n'tchito imene anayigwir chifukwa inuyo kwapano mukusangalala zot multi ndi mwana wamwamuna pa nyumbo
16:27
Machine jomo
Zachibwana heavy
Komatu kwayaka moto Ku malawi
Ngati atagawane chuma ndekut mboni ija sisamalanso mwanayotu
Munthu utha kuvomera mitala malingana ndinyengo mmene iliri...vuto ndimalemuo coz sitikuziwa kuti ankagwirizana chani ndiwantchito wawo akakhala awiri.kmanso ngati inali mitala mamuna amapanga equal popanga zithu.iwowo kod sanasiye will...
Iyeyo amayenera kumuuza mamunayo kuti amupangire tsogolo lake osati zodalira kwa mkadzi mzake zosatheka zimenezo
Koma zina